Day: July 11, 2024

Post

KUCHULUKA KWA NCHITIDWE OFALITSA MAUTHENGA ABODZA OKHUDZA MANKHWALA A HIV NDI EDZI MMASAMBA A MCHEZO

Mabungwe a National AIDS Commission (NAC) ndi Pharmacy and Medicines Regulatory Authority (PMRA) adapatsidwa mphamvu ndi malamulo yowunika ndi kuvomereza mauthenga okhudza matenda a edzi komanso kuwonetsetsa kuti mankhwala achipatala, mankhwala a zitsamba ndi zakudya kapena zakumwa zimene zili mgulu la mankhwala ndi zabwino, zotetezeka ndi zogwira ntchito bwino, komanso kuti malamulo okhudza ntchito za...