Day: January 30, 2025

Post

UNDUNA WA ZAUMOYO CHIDZIWITSO- CHITSIMIKIZO CHA KUPITILILA KUPELEKA THANDIZO LOLIMBANA NDI KACHILOMBO KA HIV NDI MATENDA A EDZI MUZIPATALA ZONSE ZA DZIKO LINO

Unduna wa zaUmoyo ukudziwitsa anthu kuti ntchito yopeleka thandizo lolimbana ndi kachilombo ka HIV lipitilila muzipatala zonse za dziko lino .Undunawu ukudziwitsa anthu kuti tili ndi mankhwala a ARV ndi mankhwala ena onse olimbana ndi kachilombo ka HIV ndi matenda a Edzi okwanila m’dziko muno. Kuonjezera apo, undunawu ukuyembekezera kulandilaso mankhwala ena ndipo upitilila kudziwitsa...

Post

MINISTRY OF HEALTH PRESS RELEASE – ASSURANCE OF SUSTAINED DELIVERY OF HIV/AIDS SERVICES IN ALL PUBLIC AND PRIVATE HEALTH FACILITIES IN MALAWI

The Ministry of Health wishes to inform the public that all HIV/AIDS services will continue to be provided normally in all the public and private health facilities across the country.The Ministry, wishes to inform the public that the country has adequate quantities of ARVs, test kits and other supplies. Further, the Ministry has put measures...