Day: June 24, 2024

WOFALITSA ZABODZA ZOKHUDZANA MACHIRITSO A HIV AWERUZIDWA KUTI AKHALE M’NDENDE MIYEZI KHUMI NDI MPHAMBU ZISANU (15)
Post

WOFALITSA ZABODZA ZOKHUDZANA MACHIRITSO A HIV AWERUZIDWA KUTI AKHALE M’NDENDE MIYEZI KHUMI NDI MPHAMBU ZISANU (15)

Bwalo la milandu laling’ono ku Mwanza lalamula a Petros Jasi kukakhala mu ndende chifukwa chonamiza anthu kuti ali ndi mankhwala omwe amachiza HIV dzina lake  ‘Gamora wochiza HIV’.                                                                                                   Masamba a Intaneti a mchezo adzadza ndi zonena za anthu ena omwe akumati ali ndi mankhwala omwe amachiza HIV omwe amatchedwa ‘Gamora wochiza HIV’. Anthuwa akhala akufalitsa...

Claimant of false HIV cure sentenced to 15 months in jail.
Post

Claimant of false HIV cure sentenced to 15 months in jail.

The Mwanza Magistrate court has passed a sentence on Mr. Petros Jasi for misinforming the public that he has medicines in the name of ‘Gamora’ that cure HIV.                                                                                                                  Social media has been awash with claims of some individuals having medication that cures HIV by the name of ‘Gamora’.The people who have been spreading the...